Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 15:26 - Buku Lopatulika

26 Ndipo anaitana mmodzi wa anyamata, namfunsa, Zinthu izi nzotani?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Ndipo anaitana mmodzi wa anyamata, namfunsa, Zinthu izi nzotani?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Adaitana wantchito mmodzi namufunsa kuti, ‘Kodi kwagwanji?’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Ndipo iye anayitana mmodzi wa antchito, namufunsa chimene chimachitika.

Onani mutuwo Koperani




Luka 15:26
4 Mawu Ofanana  

Koma mwana wake wamkulu anali kumunda. Ndipo pakubwera iye ndi kuyandikira kunyumba, anamva kuimba ndi kuvina.


Ndipo uyu anati kwa iye, Mng'ono wako wafika; ndipo atate wako anapha mwanawang'ombe wonenepa, chifukwa anamlandira iye wamoyo.


ndipo pakumva khamu la anthu alinkupita, anafunsa, Ichi nchiyani?


Ndipo anadabwa onse, nathedwa nzeru, nanena wina ndi mnzake, Kodi ichi nchiyani?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa