Luka 15:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo analakalaka kukhutitsa mimba yake ndi makoko amene nkhumba zimadya, ndipo palibe munthu anamninkha kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo analakalaka kukhutitsa mimba yake ndi makoko amene nkhumba zimadya, ndipo palibe munthu anamninkha kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Mnyamata uja ankalakalaka kudya makoko amene nkhumba zinkadya, koma panalibe munthu wompatsako ngakhale makokowo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Iye analakalaka atakhutitsa mimba yake ndi makoko amene nkhumbazo zinkadya, koma panalibe wina amene anamupatsa kanthu. Onani mutuwo |