Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 15:14 - Buku Lopatulika

14 Ndipo pamene anatha zake zonse, panakhala njala yaikulu m'dziko muja, ndipo iye anayamba kusowa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Ndipo pamene anatha zake zonse, panakhala njala yaikulu m'dziko muja, ndipo iye anayamba kusowa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Chitamthera chuma chake chonse, mudaloŵa njala yaikulu m'dziko limeneli, mwakuti iye yemwe adayamba kusauka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Iye atawononga zonse, kunagwa njala yoopsa mʼdziko lonselo ndipo anayamba kusauka.

Onani mutuwo Koperani




Luka 15:14
7 Mawu Ofanana  

Motero Yehova anawafikitsira akazembe a khamu la nkhondo la mfumu ya Asiriya, namgwira Manase ndi zokowera, nammanga matangadza, namuka naye ku Babiloni.


Wolungama adya nakhutitsa moyo wake; koma mimba ya oipa idzasowa.


Taona tsono, ndakutambasulira dzanja langa, ndi kuchepsa gawo lako la chakudya, ndi kukupereka ku chifuniro cha iwo akudana nawe, kwa ana aakazi a Afilisti akuchita manyazi ndi njira yako yoipa.


Ndipo pakupita masiku owerengeka mwana wamng'onoyo anasonkhanitsa zonse, napita ulendo wake kudziko lakutali; ndipo komweko anamwaza chuma chake ndi makhalidwe a chitayiko.


Ndipo anamuka nadziphatikiza kwa mfumu imodzi ya dziko lija; ndipo uyu anamtumiza kubusa kwake kukaweta nkhumba.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa