Luka 14:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Iye ananena fanizo kwa oitanidwa, popenya kuti amadzisankhira mipando yaulemu, nanena kwa iwo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Iye ananena fanizo kwa oitanidwa, popenya kuti amadzisankhira mipando yaulemu, nanena kwa iwo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Yesu adaaona kuti anthu amene adaaitanidwa kudzadya nao ankadzisankhira malo aulemu. Tsono adaŵaphera fanizo, adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye ataona momwe alendo amasankhira malo aulemu pa tebulo, Iye anawawuza fanizo ili: Onani mutuwo |