Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 14:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo anati kwa iwo, Ndani wa inu bulu wake kapena ng'ombe yake itagwa m'chitsime, ndipo sadzaitulutsa pomwepo tsiku la Sabata kodi?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo anati kwa iwo, Ndani wa inu bulu wake kapena ng'ombe yake itagwa m'chitsime, ndipo sadzaitulutsa pomwepo tsiku la Sabata kodi?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Kenaka adaŵafunsa kuti, “Ndani mwa inu, bulu wake kapena ng'ombe yake itagwa m'chitsime pa tsiku la Sabata, sangaitulutse pa Sabata pomwepo?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Kenaka Iye anawafunsa kuti, “Kodi ngati mmodzi mwa inu ali ndi mwana wamwamuna kapena ngʼombe imene yagwera mʼchitsime tsiku la Sabata, kodi simungamuvuwulemo tsiku lomwelo?”

Onani mutuwo Koperani




Luka 14:5
5 Mawu Ofanana  

kumasulira kwake ndi uku, mfumu; ndipo chilamuliro cha Wam'mwambamwamba chadzera mbuye wanga mfumu:


Koma Ambuye anamyankha iye, nati, Onyenga inu, kodi munthu aliyense wa inu samaimasula ng'ombe yake, kapena bulu wake ku chodyeramo, tsiku la Sabata, kupita nayo kukaimwetsa madzi?


Koma iwo anakhala chete. Ndipo anamtenga namchiritsa, namuuza apite.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa