Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 14:4 - Buku Lopatulika

4 Koma iwo anakhala chete. Ndipo anamtenga namchiritsa, namuuza apite.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Koma iwo anakhala chete. Ndipo anamtenga namchiritsa, namuuza apite.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Koma iwo adangoti chete. Tsono Yesu adatenga munthuyo, ndipo atamchiritsa, adamuuza kuti azipita.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Koma iwo sanayankhe. Tsono atamutenga munthuyo, Iye anamuchiritsa ndipo anamuwuza kuti azipita.

Onani mutuwo Koperani




Luka 14:4
4 Mawu Ofanana  

Ndipo sanalimbike mtima munthu aliyense kumfunsa kanthu kuyambira tsiku lomwelo.


Ndipo Yesu anayankha nati kwa achilamulo ndi Afarisi, nanena, Kodi nkuloledwa tsiku la Sabata kuchiritsa, kapena iai?


Ndipo anati kwa iwo, Ndani wa inu bulu wake kapena ng'ombe yake itagwa m'chitsime, ndipo sadzaitulutsa pomwepo tsiku la Sabata kodi?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa