Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 14:14 - Buku Lopatulika

14 ndipo udzakhala wodala; chifukwa iwo alibe chakubwezera iwe mphotho; pakuti idzabwezedwa mphotho pa kuuka kwa olungama.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 ndipo udzakhala wodala; chifukwa iwo alibe chakubwezera iwe mphotho; pakuti idzabwezedwa mphotho pa kuuka kwa olungama.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Apo udzakhala wodala, chifukwa iwo alibe kanthu koti nkukubwezera. Mulungu ndiye adzakubwezera, pamene anthu olungama adzauka kwa akufa.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Pamenepo udzakhala wodala, chifukwa iwo sangakubwezere kanthu, koma Mulungu ndiye adzakubwezera pa chiukitso cha olungama.”

Onani mutuwo Koperani




Luka 14:14
11 Mawu Ofanana  

Wochitira waumphawi chifundo abwereka Yehova; adzambwezera chokoma chakecho.


kotero kuti mphatso zako zachifundo zikhale zam'tseri; ndipo Atate wako wakuona m'tseri adzakubwezera iwe.


Koma pamene ukonza phwando uitane aumphawi, opunduka, otsimphina, akhungu;


nadzatulukira, amene adachita zabwino, kukuuka kwa moyo; koma amene adachita zoipa kukuuka kwa kuweruza.


ndi kukhala nacho chiyembekezo cha kwa Mulungu chimene iwo okhanso achilandira, kuti kudzakhala kuuka kwa olungama ndi osalungama.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa