Luka 13:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo onani, alipo akuthungo amene adzakhala oyamba, ndipo alipo oyamba adzakhala akuthungo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo onani, alipo akuthungo amene adzakhala oyamba, ndipo alipo oyamba adzakhala akuthungo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Pamenepo amene ali otsirizira adzakhala oyambirira, ndipo amene ali oyambirira adzakhala otsirizira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndithudi otsirizira ndiye adzakhale oyambirira, ndipo oyambirira ndiye adzakhale otsirizira.” Onani mutuwo |