Luka 13:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo munthu anati kwa Iye, Ambuye, akupulumutsidwa ndiwo owerengeka kodi? Koma Iye anati kwa iwo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo munthu anati kwa Iye, Ambuye, akupulumutsidwa ndiwo owerengeka kodi? Koma Iye anati kwa iwo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Munthu wina adamufunsa kuti, “Ambuye, kodi adzapulumuka ndi anthu oŵerengeka okha?” Yesu adayankha kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Wina anamufunsa Iye kuti, “Ambuye, kodi ndi anthu ochepa okha amene adzapulumutsidwe?” Iye anawawuza kuti, Onani mutuwo |