Luka 13:21 - Buku Lopatulika21 Ufanana ndi chotupitsa mikate, chimene mkazi anatenga, nachibisa mu miyeso itatu ya ufa, kufikira unatupo wonsewo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ufanana ndi chotupitsa mikate, chimene mkazi anatenga, nachibisa mu miyeso itatu ya ufa, kufikira unatupo wonsewo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Ulinso ngati chofufumitsira buledi, chimene mai wina adachisanganiza ndi ufa wokwanira miyeso itatu, mpaka mtanda wonse udafufuma.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Uli ngati yisiti amene mayi anatenga ndi kusakaniza ndi ufa wambiri mpaka anafufumitsa ufawo.” Onani mutuwo |