Luka 12:51 - Buku Lopatulika51 Kodi muyesa kuti ndinadzera kudzapatsa mtendere padziko lapansi? Ndinena kwa inu, Iaitu, komatu kutsutsana; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Kodi muyesa kuti ndinadzera kudzapatsa mtendere pa dziko lapansi? Ndinena kwa inu, Iaitu, komatu kutsutsana; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Kodi mukuyesa kuti ndidadzapereka mtendere pansi pano? Iyai, kunena zoona, osati mtendere koma kugaŵikana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Kodi mukuganiza kuti Ine ndinabwera kudzabweretsa mtendere pa dziko lapansi? Ayi, Ine ndikukuwuzani kuti, ndinabweretsa kugawikana. Onani mutuwo |