Luka 12:34 - Buku Lopatulika34 Pakuti kumene kuli chuma chanu, komweko kudzakhalanso mtima wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Pakuti kumene kuli chuma chanu, komweko kudzakhalanso mtima wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Pajatu kumene kuli chuma chako, mtima wakonso kokhala nkomweko.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Popeza kumene kuli chuma chanu, mtima wanunso udzakhala komweko.” Onani mutuwo |