Luka 12:30 - Buku Lopatulika30 Pakuti izi zonse mitundu ya anthu a padziko lapansi amazifunafuna; koma Atate wanu adziwa kuti musowa zimenezi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Pakuti izi zonse mitundu ya anthu a pa dziko lapansi amazifunafuna; koma Atate wanu adziwa kuti musowa zimenezi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Paja zimenezi amazifunafuna ndi anthu a mitundu yonse yapansipano. Atate anu amadziŵa kuti mumazisoŵa zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Pakuti anthu akunja amathamanga kufunafuna zinthu zotere, ndipo Atate amadziwa kuti mumazifuna zimenezi. Onani mutuwo |