Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 12:25 - Buku Lopatulika

25 Ndipo ndani wa inu, ndi kuda nkhawa angathe kuonjeza mkono pa msinkhu wake?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndipo ndani wa inu, ndi kuda nkhawa angathe kuonjeza mkono pa msinkhu wake?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Ndani mwa inu ndi maganizo ankhaŵa angathe kuwonjezera ngakhale tsiku limodzi pa moyo wake?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Ndi ndani wa inu akhoza kuwonjeza ora pa moyo wake chifukwa cha kudandaula?

Onani mutuwo Koperani




Luka 12:25
5 Mawu Ofanana  

Onani, munaika masiku anga akhale monga kuyesa dzanja; ndipo zaka zanga zili ngati chabe pamaso panu, Indedi munthu aliyense angakhale wokhazikika, ali chabe konse.


Kapena usalumbire kumutu wako, chifukwa sungathe kuliyeretsa mbuu kapena kulidetsa bii tsitsi limodzi.


Ndipo ndani wa inu ndi kudera nkhawa angathe kuonjezera pa msinkhu wake mkono umodzi?


Kotero ngati simungathe ngakhale chaching'onong'ono, muderanji nkhawa chifukwa cha zina zija?


Ndipo anafuna kuona Yesu ndiye uti, ndipo sanathe, chifukwa cha khamulo, pakuti anali wamfupi msinkhu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa