Luka 12:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Iye ananena nao fanizo, kuti, Munda wake wa munthu mwini chuma unapatsa bwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Iye ananena nao fanizo, kuti, Munda wake wa munthu mwini chuma unapatsa bwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono Yesu adaŵaphera fanizo. Adati, “Munthu wina wachuma m'munda mwake mudabereka dzinthu dzambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndipo Iye anawawuza fanizo ili, “Munda wa munthu wina wachuma unabereka kwambiri. Onani mutuwo |