Luka 11:6 - Buku Lopatulika6 popeza wandidzera bwenzi langa lochokera paulendo ndipo ndilibe chompatsa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 popeza wandidzera ndipo ndilibe chompatsa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Kwafika bwenzi langa, ali pa ulendo, ndipo ndilibe choti ndingampatse.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 chifukwa ndalandira bwenzi langa amene ali pa ulendo ndipo ine ndilibe choti ndimupatse.’ Onani mutuwo |