Luka 11:47 - Buku Lopatulika47 Tsoka inu! Chifukwa mumanga za pa manda a aneneri, ndipo makolo anu anawapha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Tsoka inu! Chifukwa mumanga za pa manda a aneneri, ndipo makolo anu anawapha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Muli ndi tsoka, chifukwa mumamanga ziliza za aneneri, pamene ndi makolo anu omwe akale amene adapha aneneriwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 “Tsoka kwa inu, chifukwa mumawaka manda a aneneri, komatu ndi makolo anu amene anawapha. Onani mutuwo |