Luka 11:44 - Buku Lopatulika44 Tsoka inu! Chifukwa muli ngati manda osaoneka, ndipo anthu akuyendayenda pamwamba pao sadziwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Tsoka inu! Chifukwa muli ngati manda osaoneka, ndipo anthu akuyendayenda pamwamba pao sadziwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Muli ndi tsoka, chifukwa muli ngati manda osazindikirika, amene anthu amapondapo osadziŵa kanthu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 “Tsoka kwa inu Afarisi, chifukwa muli ngati manda osawaka, amene anthu amangoyendapo, osawadziwa.” Onani mutuwo |