Luka 11:43 - Buku Lopatulika43 Tsoka inu, Afarisi! Chifukwa mukonda mipando yaulemu m'masunagoge, ndi kupatsidwa moni m'misika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Tsoka inu, Afarisi! Chifukwa mukonda mipando yaulemu m'masunagoge, ndi kupatsidwa moni m'misika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Muli ndi tsoka, inu Afarisi, chifukwa mumakonda mipando yaulemu m'nyumba zamapemphero, ndiponso kuti anthu azikupatsani moni waulemu pa misika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 “Tsoka kwa inu Afarisi, chifukwa mumakonda mipando yofunika kwambiri mʼmasunagoge ndi malonje mʼmalo a pa msika. Onani mutuwo |