Luka 11:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo mutikhululukire ife machimo athu; pakuti ifenso tikhululukira munthu yense wa mangawa athu. Ndipo musatitengere ife kokatiyesa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo mutikhululukire ife machimo athu; pakuti ifenso tikhululukira munthu yense wa mangawa athu. Ndipo musatitengere ife kokatiyesa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mutikhululukire ife machimo athu, pakuti ifenso timakhululukira aliyense wotilakwira. Ndipo musalole kuti tigwe m'zotiyesa.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 mutikhululukire machimo athu, monga ifenso timakhululukira aliyense amene watilakwira. Ndipo musalole kuti tigwe mʼmayesero.’ ” Onani mutuwo |