Luka 11:21 - Buku Lopatulika21 Pamene paliponse mwini mphamvu alonda pabwalo pake zinthu zake zili mumtendere; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pamene paliponse mwini mphamvu alonda pabwalo pake zinthu zake zili mumtendere; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 “Munthu wamphamvu akamalonda nyumba yake ali ndi zida zankhondo, katundu wake amakhala pabwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 “Munthu wamphamvu, amene ali ndi zida, akamalondera nyumba yake, katundu wake amatetezedwa. Onani mutuwo |