Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 11:16 - Buku Lopatulika

16 Koma ena anamuyesa, nafuna kwa Iye chizindikiro chochokera Kumwamba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Koma ena anamuyesa, nafuna kwa Iye chizindikiro chochokera Kumwamba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Enanso pofuna kumuyesa, adampempha kuti aŵaonetse chizindikiro chozizwitsa chochokera kumwamba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Ena anamuyesa pomufunsa chizindikiro chochokera kumwamba.

Onani mutuwo Koperani




Luka 11:16
7 Mawu Ofanana  

Ndipo pakusonkhana pamodzi makamu a anthu, anayamba kunena, Mbadwo uno ndi mbadwo woipa; ufuna chizindikiro, ndipo chizindikiro sichidzapatsidwa kwa uwu koma chizindikiro cha Yona.


Chifukwa chake anati kwa Iye, Ndipo muchita chizindikiro chanji, kuti tione ndi kukhulupirira Inu? Muchita chiyani?


Koma ichi ananena kuti amuyese Iye, kuti akhale nacho chomneneza Iye. Koma Yesu, m'mene adawerama pansi analemba pansi ndi chala chake.


Ndipo popeza Ayuda afunsa zizindikiro, ndi Agriki atsata nzeru:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa