Luka 10:9 - Buku Lopatulika9 ndipo chiritsani odwala ali momwemo nimunene nao, Ufumu wa Mulungu wayandikira kwa inu. Koma kumudzi uliwonse mukalowako, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 ndipo chiritsani odwala ali momwemo nimunene nao, Ufumu wa Mulungu wayandikira kwa inu. Koma kumudzi uliwonse mukalowako, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Muchiritse anthu odwala amene ali m'mudzimo, ndipo muŵauze kuti, ‘Tsopano ufumu wa Mulungu wakufikirani.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Chiritsani odwala amene ali kumeneko ndipo muwawuze kuti, ‘Ufumu wa Mulungu wayandikira.’ Onani mutuwo |