Luka 10:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo m'mudzi uliwonse mukalowamo, ndipo alandira inu, idyani zomwezi akupatsani; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo m'mudzi uliwonse mukalowamo, ndipo alandira inu, idyani zomwezi akupatsani; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mukaloŵa m'mudzi, anthu nakulandirani, mudye zimene akukonzerani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Mukamalowa mʼmudzi, ndi kulandiridwa, idyani chilichonse akukonzerani. Onani mutuwo |