Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 10:10 - Buku Lopatulika

10 ndipo salandira inu, m'mene mwatuluka kumakwalala ake nenani,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 ndipo salandira inu, m'mene mwatuluka kumakwalala ake nenani,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Koma kumudzi kumene mukaloŵe, anthu nkupanda kukulandirani bwino, mukapite m'miseu yam'mudzimo, nkukanena kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Koma mukalowa mʼmudzi ndipo osalandiridwa bwino, kapiteni ku misewu mʼmudzimo nʼkukanena kuti,

Onani mutuwo Koperani




Luka 10:10
7 Mawu Ofanana  

Ndipo iwowa, ngakhale akamva kapena akaleka kumva, (pakuti ndiwo nyumba yopanduka,) koma adzadziwa kuti panali mneneri pakati pao.


Ndipo yemwe sadzakulandirani inu kapena kusamva mau anu, pamene mulikutuluka m'nyumbayo, kapena m'mudzimo, sansani fumbi m'mapazi anu.


Lingakhale fumbi lochokera kumudzi kwanu, lomamatika kumapazi athu, tilisansira pa inu; koma zindikirani ichi, kuti Ufumu wa Mulungu wayandikira.


ndipo chiritsani odwala ali momwemo nimunene nao, Ufumu wa Mulungu wayandikira kwa inu. Koma kumudzi uliwonse mukalowako,


Ndipo onse amene sakakulandireni inu, m'mene mutuluka m'mudzi womwewo, sansani fumbi la pa mapazi anu, likhale mboni ya paiwo.


Koma iwo, m'mene adawasansira fumbi la ku mapazi ao anadza ku Ikonio.


Koma pamene iwo, anamkana, nachita mwano, anakutumula malaya ake, nati kwa iwo, Mwazi wanu ukhale pa mitu yanu; ine ndilibe kanthu; kuyambira tsopano ndinka kwa amitundu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa