Luka 10:29 - Buku Lopatulika29 Koma iye, pofuna kudziyesa yekha wolungama, anati kwa Yesu, Ndipo mnansi wanga ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Koma iye, pofuna kudziyesa yekha wolungama, anati kwa Yesu, Ndipo mnansi wanga ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Koma munthu uja pofuna kudziwonetsa ngati wolungama, adafunsa Yesu kuti, “Nanga mnzangayo ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Koma iye anafuna kudzilungamitsa yekha, ndipo anamufunsanso Yesu kuti, “Kodi mnansi wanga ndani?” Onani mutuwo |