Luka 1:74 - Buku Lopatulika74 Kutipatsa ife kuti titalanditsidwa kudzanja la adani athu, tidzamtumikira Iye, opanda mantha, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201474 Kutipatsa ife kuti titalanditsidwa kudzanja la adani athu, tidzamtumikira Iye, opanda mantha, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa74 kuti adzatipulumutsa kwa adani athu, kuti tizimtumikira mopanda mantha, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero74 kutilanditsa ife mʼdzanja la adani athu, ndi kutipanga ife timutumikire Iye mopanda mantha, Onani mutuwo |