Luka 1:62 - Buku Lopatulika62 Ndipo anakodola atate wake, afuna amutche dzina liti? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201462 Ndipo anakodola atate wake, afuna amutche dzina liti? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa62 Tsono adalankhula ndi bambo wake ndi manja, namufunsa kuti, “Mukufuna kuti timutche dzina lanji?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero62 Pamenepo anapanga zizindikiro kwa abambo ake kuti adziwe dzina limene akanakonda kumutcha mwanayo. Onani mutuwo |