Luka 1:61 - Buku Lopatulika61 Ndipo iwo anati kwa iye, Palibe wina wa abale ako amene atchedwa dzina ili. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201461 Ndipo iwo anati kwa iye, Palibe wina wa abale ako amene atchedwa dzina ili. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa61 Pamenepo anthuwo adamuuza kuti, “Koma pakati pa abale anu palibe amene ali ndi dzina limeneli.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero61 Iwo anati kwa iye, “Palibe mmodzi mwa abale ake amene ali ndi dzina limeneli.” Onani mutuwo |