Luka 1:60 - Buku Lopatulika60 Ndipo amake anayankha, kuti, Iai; koma adzatchedwa Yohane. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201460 Ndipo amake anayankha, kuti, Iai; koma adzatchedwa Yohane. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa60 Koma mai wake adakana, adati, “Iyai, koma atchedwe Yohane.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero60 koma amayi ake anayankhula nati, “Ayi, atchulidwe kuti Yohane.” Onani mutuwo |