Luka 1:59 - Buku Lopatulika59 Ndipo panali tsiku lachisanu ndi chitatu iwo anadza kudzadula kamwanako; ndipo akati amutche dzina la atate wake Zekariya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201459 Ndipo panali tsiku lachisanu ndi chitatu iwo anadza kudzadula kamwanako; ndipo akati amutche dzina la atate wake Zekariya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa59 Pa tsiku lachisanu ndi chitatu mwanayo atabadwa, adadza naye kuti amuumbale, nafuna kumutcha dzina la bambo wake Zakariya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero59 Pa tsiku lachisanu ndi chitatu anabwera ndi mwana kuti adzachitidwe mdulidwe, ndipo anafuna kumupatsa dzina la abambo ake Zakariya, Onani mutuwo |