Luka 1:63 - Buku Lopatulika63 Ndipo iye anafunsa cholemberapo, nalemba, kuti, Dzina lake ndi Yohane. Ndipo anazizwa onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201463 Ndipo iye anafunsa cholemberapo, nalemba, kuti, Dzina lake ndi Yohane. Ndipo anazizwa onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa63 Zakariya adapempha cholemberapo, nalembapo kuti, “Dzina lake ndi Yohane.” Anthu onsewo adazizwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero63 Iye anapempha poti alembepo, ndipo chodabwitsa kwa aliyense analemba kuti, “Dzina lake ndi Yohane.” Onani mutuwo |