Luka 1:56 - Buku Lopatulika56 Ndipo Maria anakhala ndi iye ngati miyezi itatu, nabweranso kunyumba kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201456 Ndipo Maria anakhala ndi iye ngati miyezi itatu, nabweranso kunyumba kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa56 Maria atakhala ndi Elizabeti ngati miyezi itatu, adabwerera kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero56 Mariya anakhala ndi Elizabeti pafupifupi miyezi itatu ndipo kenaka anabwerera kwawo. Onani mutuwo |