Luka 1:53 - Buku Lopatulika53 Anawakhutitsa anjala ndi zinthu zabwino, ndipo eni chuma anawachotsa opanda kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Anawakhutitsa anjala ndi zinthu zabwino, ndipo eni chuma anawachotsa opanda kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Anthu anjala waŵakhutitsa ndi zabwino, anthu olemera nkuŵabweza osaŵapatsa kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Iye wakhutitsa a njala ndi zinthu zabwino koma anachotsa olemera wopanda kanthu. Onani mutuwo |