Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 1:52 - Buku Lopatulika

52 Iye anatsitsa mafumu pa mipando yao yachifumu, ndipo anakweza aumphawi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

52 Iye anatsitsa mafumu pa mipando yao yachifumu, ndipo anakweza aumphawi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

52 Mafumu amphamvu waŵatsitsa pa mipando yao yachifumu, anthu wamba nkuŵakweza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

52 Iye anachotsa olamulira pa mipando yawo yaufumu, koma wakweza odzichepetsa.

Onani mutuwo Koperani




Luka 1:52
14 Mawu Ofanana  

Pakuti atuluka m'nyumba yandende kulowa ufumu; komanso yemwe abadwa m'dziko lake asauka.


Ndipo mitengo yonse yakuthengo idzadziwa kuti Ine Yehova ndatsitsa mtengo wosomphoka, ndakuza mtengo waung'ono, ndaumitsa mtengo wauwisi, ndi kuphukitsa mtengo wouma; Ine Yehova ndanena ndi kuchichita.


Tsiku lomwelo ndidzautsa msasa wa Davide udagwawo, ndi kukonzanso zopasuka zake; ndipo ndidzautsa zogumuka zake, ndi kuumanga monga masiku a kalelo;


Si mmisiri wa mitengo uyu, mwana wa Maria, mbale wao wa Yakobo, ndi Yose, ndi Yudasi, ndi Simoni? Ndipo alongo ake sali nafe pano kodi? Ndipo anakhumudwa ndi Iye.


Chifukwa munthu aliyense wakudzikuza adzachepetsedwa; ndipo wakudzichepetsa adzakulitsidwa.


Ndinena ndi inu, anatsikira kunyumba kwake woyesedwa wolungama uyutu, wosati uja ai; pakuti yense wakudzikuza yekha adzachepetsedwa; koma wodzichepetsa yekha adzakulitsidwa.


Dzichepetseni pamaso pa Ambuye, ndipo adzakukwezani.


Mauta a amphamvu anathyoka, koma okhumudwawo amangiridwa ndi mphamvu m'chuuno.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa