Luka 1:47 - Buku Lopatulika47 ndipo mzimu wanga wakondwera mwa Mulungu Mpulumutsi wanga, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 ndipo mzimu wanga wakondwera mwa Mulungu Mpulumutsi wanga, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 ndipo mzimu wanga ukukondwera mwa Mulungu, Mpulumutsi wanga, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Ndipo mzimu wanga ukondwera mwa Mulungu Mpulumutsi wanga, Onani mutuwo |