Luka 1:45 - Buku Lopatulika45 Ndipo wodala ali iye amene anakhulupirira; chifukwa zidzachitidwa zinthu zimene Ambuye analankhula naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Ndipo wodala ali iye amene anakhulupirira; chifukwa zidzachitidwa zinthu zimene Ambuye analankhula naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Ndinu odala chifukwa mudakhulupirira kuti zimene Ambuye adakuuzani, zidzachitadi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Wodala iye amene wakhulupirira kuti chimene Ambuye wanena kwa iye chidzakwaniritsidwa!” Onani mutuwo |