Luka 1:44 - Buku Lopatulika44 Pakuti ona, pamene mau a moni wako analowa m'makutu anga, mwana anatsalima ndi msangalalo m'mimba mwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Pakuti ona, pamene mau a moni wako analowa m'makutu anga, mwana anatsalima ndi msangalalo m'mimba mwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Chifukwatu pamene ndinamva malonje anu, mwana anayamba kutakataka ndi chimwemwe m'mimba mwanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Nthawi yomwe ndinamva mawu akulonjera kwanu, mwana anatakataka mʼmimba mwanga chifukwa cha chimwemwe. Onani mutuwo |