Luka 1:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo Maria anati, Onani, mdzakazi wa Ambuye; kukhale kwa ine monga mwa mau anu. Ndipo mngelo anachoka kwa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo Maria anati, Onani, mdzakazi wa Ambuye; kukhale kwa ine monga mwa mau anu. Ndipo mngelo anachoka kwa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Apo Maria adati, “Ndine mtumiki wa Ambuye; zindichitikire monga mwaneneramo.” Ndipo mngeloyo adamsiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Mariya anayankha kuti, “Ine ndine mtumiki wa Ambuye. Zikhale kwa ine monga mwanenera.” Onani mutuwo |