Luka 1:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo Maria ananyamuka masiku amenewa, namuka ndi changu kudziko la mapiri kumzinda wa Yuda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo Maria ananyamuka masiku amenewa, namuka ndi changu kudziko la mapiri kumudzi wa Yuda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Patapita masiku oŵerengeka, Maria adanyamuka napita mofulumira ku dera lamapiri, ku mudzi wina wa ku Yudeya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Nthawi imeneyo anakonzeka ndipo anapita mofulumira ku mudzi wa ku mapiri a dziko la Yudeya, Onani mutuwo |