Luka 1:29 - Buku Lopatulika29 Koma iye ananthunthumira ndi mau awa, nasinkhasinkha kulonjera uku nkutani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Koma iye ananthunthumira ndi mau awa, nasinkhasinkha kulonjera uku nkutani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Maria adadzidzimuka nawo kwambiri mau ameneŵa, nayamba kusinkhasinkha kuti kodi moni umenewu ndi wa mtundu wanji? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Mariya anavutika kwambiri ndi mawu awa ndipo anadabwa ndi kulonjera kotere. Onani mutuwo |