Luka 1:25 - Buku Lopatulika25 Ambuye wandichitira chotero m'masiku omwe Iye anandipenyera, kuchotsa manyazi anga pakati pa anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ambuye wandichitira chotero m'masiku omwe Iye anandipenyera, kuchotsa manyazi anga pakati pa anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Adati, “Ambuye andichitira zotere: nthaŵi inoyi andiwonetsa chifundo chao, andichotsa manyazi pakati pa anthu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Iye anati, “Ambuye wandichitira izi, kuti mʼmasiku ano wandionetsera kukoma mtima kwake ndi kuchotsa manyazi anga pakati pa anthu.” Onani mutuwo |