Luka 1:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo mwezi wachisanu ndi chimodzi mngelo Gabriele anatumidwa ndi Mulungu kunka kumzinda wa ku Galileya dzina lake Nazarete, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo mwezi wachisanu ndi chimodzi mngelo Gabriele anatumidwa ndi Mulungu kunka kumudzi wa ku Galileya dzina lake Nazarete, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Elizabeti ali ndi pathupi pa miyezi isanu ndi umodzi, Mulungu adatuma mngelo Gabriele ku mudzi wina wa ku Galileya, dzina lake Nazarete. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Mwezi wachisanu ndi chimodzi, Mulungu anatuma mngelo Gabrieli ku Nazareti, mudzi wa ku Galileya, Onani mutuwo |