Luka 1:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anamuonekera iye mngelo wa Ambuye, naimirira kudzanja lamanja la guwa la nsembe la zonunkhira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anamuonekera iye mngelo wa Ambuye, naimirira kudzanja lamanja la guwa la nsembe la zonunkhira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono mngelo wa Ambuye adaonekera Zakariya. Mngeloyo adaaimirira ku dzanja lamanja la guwa lofukizirapo lubani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kenaka mngelo wa Ambuye anaonekera kwa iye, atayimirira ku dzanja lamanja la guwa lofukizira. Onani mutuwo |