Luka 1:1 - Buku Lopatulika1 Popeza ambiri anayesa kulongosola nkhani ya zinthu zinachitika pakati pa ife, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Popeza ambiri anayesa kulongosola nkhani ya zinthu zinachitika pakati pa ife, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ateofilo olemekezeka, Anthu ambiri adayesa kulongosola mbiri ya zinthu zimene zidachitika pakati pathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ambiri anayesa kufotokoza nkhani ya zimene zinakwaniritsidwa pakati pathu, Onani mutuwo |