Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 9:8 - Buku Lopatulika

8 Pamenepo Aroni anasendera kufupi kwa guwa la nsembe, napha mwanawang'ombe wa nsembe yauchimo, ndiyo ya kwa iye yekha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Pamenepo Aroni anasendera kufupi kwa guwa la nsembe, napha mwanawang'ombe wa nsembe yauchimo, ndiyo ya kwa iye yekha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Choncho Aroni adasendera pafupi ndi guwa, napha mwanawang'ombe woperekera nsembe yopepesera machimo, nsembeyo ya iye mwini wake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Choncho Aaroni anasendera pafupi ndi guwa, napha mwana wangʼombe uja kukhala nsembe yake yopepesera machimo.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 9:8
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Aroni analankhula ndi Mose, nati, Taonani, lero abwera nayo nsembe yao yauchimo ndi nsembe yao yopsereza pamaso pa Yehova; ndipo zandigwera zotere; ndikadadya nsembe yauchimo lero, kukadakomera kodi pamaso pa Yehova?


Aike dzanja lake pamutu pa nsembe yauchimo, naiphe nsembe yauchimo pamalo pa nsembe yopsereza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa