Levitiko 9:2 - Buku Lopatulika2 ndipo anati kwa Aroni, Dzitengere mwanawang'ombe wamwamuna, akhale nsembe yauchimo, ndi nkhosa yamphongo ikhale nsembe yopsereza, zopanda chilema, nubwere nazo pamaso pa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ndipo anati kwa Aroni, Dzitengere mwanawang'ombe wamwamuna, akhale nsembe yauchimo, ndi nkhosa yamphongo ikhale nsembe yopsereza, zopanda chilema, nubwere nazo pamaso pa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adauza Aroniyo kuti, “Utenge mwanawang'ombe wamphongo kuti akhale nsembe yopepesera machimo, ndi nkhosa yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza. Zonsezo zikhale zopanda chilema, ndipo uzipereke pamaso pa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo anawuza Aaroni kuti, “Tenga mwana wangʼombe wamwamuna kuti akhale nsembe yako yopepesera machimo ndi nkhosa yayimuna kuti ikhale nsembe yopsereza. Zonsezi zikhale zopanda chilema ndipo uzipereke pamaso pa Yehova. Onani mutuwo |