Levitiko 7:4 - Buku Lopatulika4 ndi impso ziwiri, ndi mafuta a pamenepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndi impso ziwiri, ndi mafuta a pamenepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Aperekenso imso ziŵiri pamodzi ndi mafuta ake omwe cham'chiwunomu, ndiponso mphumphu ya mafuta akuchiŵindi ochotsa ndi imso zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Aperekenso impsyo ziwiri, mafuta ake pamodzi ndi mafuta onse amene ali chamʼchiwuno, ndiponso mafuta onse amene aphimba chiwindi. Onani mutuwo |