Levitiko 7:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo nsembe zonse zaufa zosakaniza ndi mafuta, kapena zouma zikhale za ana onse a Aroni, alandireko onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo nsembe zonse zaufa zosanganiza ndi mafuta, kapena zouma zikhale za ana onse a Aroni, alandireko onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ndipo chopereka chilichonse cha chakudya chosakaniza ndi mafuta kapena chouma, chikhale cha ana onse a Aroni. Anawo aigaŵane molingana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo chopereka china chilichonse cha chakudya chosakaniza ndi mafuta kapena chowuma, chikhale cha ana onse a Aaroni ndipo anawo achigawane mofanana. Onani mutuwo |