Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Levitiko 5:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo adze nazo kwa wansembe, ndiye ayambe kubwera nayo ija ya kwa nsembe yauchimo, napotole mutu wake pakhosi pake, osauchotsa;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo adze nazo kwa wansembe, ndiye ayambe kubwera nayo ija ya kwa nsembe yauchimo, napotole mutu wake pakhosi pake, osauchotsa;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Abwere nazo kwa wansembe, ndipo wansembeyo ayambe wapereka mbalame yopepesera machimoyo. Aipotole khosi, koma asaidule mutu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Tsono abwere nazo kwa wansembe, ndipo wansembeyo ayambe wapereka mbalame imodzi ngati yopepesera tchimo. Apotole khosi koma osayidula mutu,

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 5:8
4 Mawu Ofanana  

Ndipo wansembe abwere nacho ku guwa la nsembe, namwetule mutu wake, naitenthe paguwa la nsembe; ndi mwazi wake aukamulire pa mbali ya guwa la nsembe,


nang'ambe mapiko ake osawachotsa konse ai; ndipo wansembeyo aitenthe paguwa la nsembe, pa nkhuni zili pamoto; ndiyo nsembe yopsereza, nsembe yamoto, ya fungo lokoma la kwa Yehova.


amene anaperekedwa chifukwa cha zolakwa zathu, naukitsidwa chifukwa cha kutiyesa ife olungama.


Pakuti Khristunso adamva zowawa kamodzi, chifukwa cha machimo, wolungama m'malo mwa osalungama, kuti akatifikitse kwa Mulungu; wophedwatu m'thupi, koma wopatsidwa moyo mumzimu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa